14 Sindidzaimba mlandu ana anu aakazi chifukwa cha chiwerewere chawo,
Komanso akazi a ana anu chifukwa cha chigololo chawo.
Chifukwa amuna akuyenda ndi mahule
Ndipo amapereka nsembe limodzi ndi mahule apakachisi.
Anthu osamvetsa zinthu amenewa+ adzawonongedwa.