Hoseya 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngakhale kuti inu Aisiraeli mukuchita chiwerewere,+Yuda asakhale ndi mlandu.+ Musabwere ku Giligala+ kapena ku Beti-aveni,+Ndipo musalumbire kuti, ‘Mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo!’+
15 Ngakhale kuti inu Aisiraeli mukuchita chiwerewere,+Yuda asakhale ndi mlandu.+ Musabwere ku Giligala+ kapena ku Beti-aveni,+Ndipo musalumbire kuti, ‘Mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo!’+