Hoseya 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Isiraeli wakhala wamakani ngati ngʼombe yomwe ikuchita makani.+ Ndiye kodi Yehova adzawaweta ngati nkhosa yamphongo yaingʼono pamalo odyetsera ziweto?
16 Isiraeli wakhala wamakani ngati ngʼombe yomwe ikuchita makani.+ Ndiye kodi Yehova adzawaweta ngati nkhosa yamphongo yaingʼono pamalo odyetsera ziweto?