Hoseya 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kunyada kwa Isiraeli kwakhala umboni womutsutsa,+Ndipo Isiraeli ndi Efuraimu apunthwa ndi zolakwa zawo.Nayenso Yuda wapunthwa nawo limodzi.+
5 Kunyada kwa Isiraeli kwakhala umboni womutsutsa,+Ndipo Isiraeli ndi Efuraimu apunthwa ndi zolakwa zawo.Nayenso Yuda wapunthwa nawo limodzi.+