-
Hoseya 6:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ife tidzamudziwa Yehova ndipo tidzayesetsa kuti timudziwe bwino.
Nʼzosakayikitsa kuti adzatulukira ngati mmene mʼbandakucha umafikira.
Adzabwera kwa ife ngati mvula yambiri,
Ngati mvula yomalizira imene imanyowetsa kwambiri nthaka.”
-