Hoseya 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Gulu la ansembe lili ngati gulu la achifwamba lobisalira munthu panjira. Amapha anthu mumsewu ku Sekemu+Chifukwa khalidwe lawo ndi lochititsa manyazi.
9 Gulu la ansembe lili ngati gulu la achifwamba lobisalira munthu panjira. Amapha anthu mumsewu ku Sekemu+Chifukwa khalidwe lawo ndi lochititsa manyazi.