Hoseya 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma mumtima mwawo saganiza nʼkomwe kuti ndidzakumbukira zoipa zawo zonse.+ Tsopano zochita zawo zawazungulira.Ndipo zili pamaso panga.
2 Koma mumtima mwawo saganiza nʼkomwe kuti ndidzakumbukira zoipa zawo zonse.+ Tsopano zochita zawo zawazungulira.Ndipo zili pamaso panga.