-
Hoseya 7:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Anthu onsewo ndi achigololo.
Ali ngati uvuni imene wophika mkate wayatsa.
Ndipo wasiya kuisonkhezera pamene akudikira kuti ufa umene wakanda ufufume.
-