Hoseya 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Onsewo akutentha ngati uvuni wamoto,Ndipo amameza atsogoleri* awo. Mafumu awo onse agwa.+Palibe aliyense amene akundiitana.+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:7 Nsanja ya Olonda,3/1/1989, tsa. 14
7 Onsewo akutentha ngati uvuni wamoto,Ndipo amameza atsogoleri* awo. Mafumu awo onse agwa.+Palibe aliyense amene akundiitana.+