Hoseya 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kunyada kwa Aisiraeli kwakhala umboni wowatsutsa,+Koma iwo sanabwerere kwa Yehova Mulungu wawo.+Ndiponso sanamufunefune ngakhale kuti pali zonsezi.
10 Kunyada kwa Aisiraeli kwakhala umboni wowatsutsa,+Koma iwo sanabwerere kwa Yehova Mulungu wawo.+Ndiponso sanamufunefune ngakhale kuti pali zonsezi.