Hoseya 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu a ku Efuraimu ali ngati nkhunda yopusa, yopanda nzeru.+ Iwo apempha thandizo ku Iguputo+ ndiponso apita kudziko la Asuri.+
11 Anthu a ku Efuraimu ali ngati nkhunda yopusa, yopanda nzeru.+ Iwo apempha thandizo ku Iguputo+ ndiponso apita kudziko la Asuri.+