Hoseya 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kulikonse kumene iwo angapite, ndidzawatchera ukonde. Ndidzawagwira ngati mbalame zouluka mumlengalenga. Ndidzawalanga mogwirizana ndi chenjezo limene ndinkawauza ndikawasonkhanitsa.+
12 Kulikonse kumene iwo angapite, ndidzawatchera ukonde. Ndidzawagwira ngati mbalame zouluka mumlengalenga. Ndidzawalanga mogwirizana ndi chenjezo limene ndinkawauza ndikawasonkhanitsa.+