Hoseya 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ika lipenga la nyanga ya nkhosa pakamwa pako.+ Mdani akubwera ngati chiwombankhanga kudzaukira nyumba ya Yehova.+Chifukwa Aisiraeli aphwanya pangano langa+ ndiponso sanatsatire malamulo anga.+
8 “Ika lipenga la nyanga ya nkhosa pakamwa pako.+ Mdani akubwera ngati chiwombankhanga kudzaukira nyumba ya Yehova.+Chifukwa Aisiraeli aphwanya pangano langa+ ndiponso sanatsatire malamulo anga.+