Hoseya 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo akungofesa mphepo,Ndipo adzakolola mphepo yamkuntho.+ Mbewu zawo sizidzakula mpaka kukhwima.+Ndipo zimene zidzakule, sizidzawapatsa ufa. Ngati zina zingabereke, alendo adzazimeza.+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:7 Nsanja ya Olonda,11/15/2005, tsa. 26
7 Iwo akungofesa mphepo,Ndipo adzakolola mphepo yamkuntho.+ Mbewu zawo sizidzakula mpaka kukhwima.+Ndipo zimene zidzakule, sizidzawapatsa ufa. Ngati zina zingabereke, alendo adzazimeza.+