Hoseya 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndinamulembera zinthu zambiri zokhudza malamulo* anga,Koma anangoziona ngati zachilendo.+