Hoseya 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwo amapereka nsembe kwa ine ndipo amadya nyama yake,Koma ine Yehova sindikondwera nazo.+ Tsopano ndidzakumbukira zolakwa zawo ndipo ndidzawalanga chifukwa cha machimo awo.+ Iwo anabwerera* ku Iguputo.+
13 Iwo amapereka nsembe kwa ine ndipo amadya nyama yake,Koma ine Yehova sindikondwera nazo.+ Tsopano ndidzakumbukira zolakwa zawo ndipo ndidzawalanga chifukwa cha machimo awo.+ Iwo anabwerera* ku Iguputo.+