Hoseya 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Isiraeli anaiwala amene anamupanga+ ndipo wamanga akachisi.+Yuda nayenso wamanga mizinda yambiri yokhala ndi mipanda yolimba.+ Koma ine ndidzatumiza moto mʼmizinda yakeNdipo udzawotcha nsanja zamumzinda uliwonse.”+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:14 Nsanja ya Olonda,9/15/2007, tsa. 16 Tsiku la Yehova, ptsa. 59-61
14 Isiraeli anaiwala amene anamupanga+ ndipo wamanga akachisi.+Yuda nayenso wamanga mizinda yambiri yokhala ndi mipanda yolimba.+ Koma ine ndidzatumiza moto mʼmizinda yakeNdipo udzawotcha nsanja zamumzinda uliwonse.”+