Hoseya 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Usasangalale iwe Isiraeli.+Usachite zinthu mosangalala ngati anthu a mitundu ina. Popeza wasiya Mulungu wako chifukwa cha chiwerewere.+ Umakonda kulandira malipiro a uhule wako pamalo onse opunthira mbewu.+
9 “Usasangalale iwe Isiraeli.+Usachite zinthu mosangalala ngati anthu a mitundu ina. Popeza wasiya Mulungu wako chifukwa cha chiwerewere.+ Umakonda kulandira malipiro a uhule wako pamalo onse opunthira mbewu.+