Hoseya 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwe sudzapitiriza kukhala mʼdziko la Yehova.+Mʼmalomwake Efuraimu adzabwerera ku Iguputo,Ndipo adzadya zinthu zodetsedwa kudziko la Asuri.+
3 Iwe sudzapitiriza kukhala mʼdziko la Yehova.+Mʼmalomwake Efuraimu adzabwerera ku Iguputo,Ndipo adzadya zinthu zodetsedwa kudziko la Asuri.+