-
Hoseya 9:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Chifukwa zili ngati chakudya chapamaliro.
Onse amene adzadya chakudyacho adzadzidetsa.
Chakudya chake chidzangokhala cha iyeyo basi,
Ndipo sichidzalowa mʼnyumba ya Yehova.
-