Hoseya 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Zoipa zawo zonse zinachitikira ku Giligala,+ ndipo ndinadana nawo kumeneko. Chifukwa cha zochita zawo zoipa, ndidzawathamangitsa panyumba yanga.+ Ndipo sindidzawakondanso.+Akalonga awo onse ndi amakani.
15 “Zoipa zawo zonse zinachitikira ku Giligala,+ ndipo ndinadana nawo kumeneko. Chifukwa cha zochita zawo zoipa, ndidzawathamangitsa panyumba yanga.+ Ndipo sindidzawakondanso.+Akalonga awo onse ndi amakani.