Hoseya 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Isiraeli ndi mtengo wa mpesa wowonongeka* umene ukubereka zipatso.+ Pamene zipatso zake zikuchuluka, mʼpamenenso akumanga maguwa ambiri.+Pamene zokolola zikuchuluka mʼdziko lake, mʼpamenenso akumanga zipilala zopatulika zokongola kwambiri.+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:1 Nsanja ya Olonda,11/15/2005, tsa. 27
10 “Isiraeli ndi mtengo wa mpesa wowonongeka* umene ukubereka zipatso.+ Pamene zipatso zake zikuchuluka, mʼpamenenso akumanga maguwa ambiri.+Pamene zokolola zikuchuluka mʼdziko lake, mʼpamenenso akumanga zipilala zopatulika zokongola kwambiri.+