Hoseya 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo amalankhula mawu opanda nzeru, amalumbira monama+ ndiponso amachita mapangano.Choncho chiweruzo chimene chikubwera chili ngati zomera zapoizoni mʼmunda.+
4 Iwo amalankhula mawu opanda nzeru, amalumbira monama+ ndiponso amachita mapangano.Choncho chiweruzo chimene chikubwera chili ngati zomera zapoizoni mʼmunda.+