Hoseya 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Malo okwezeka a ku Beti-aveni,+ omwe ndi tchimo la Isiraeli,+ adzawonongedwa.+ Minga ndi zitsamba zobaya zidzamera pamaguwa awo ansembe.+ Anthu adzauza mapiri kuti, ‘Tikwirireni!’ Adzauzanso mapiri angʼonoangʼono kuti, ‘Tigwereni!’+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:8 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 112
8 Malo okwezeka a ku Beti-aveni,+ omwe ndi tchimo la Isiraeli,+ adzawonongedwa.+ Minga ndi zitsamba zobaya zidzamera pamaguwa awo ansembe.+ Anthu adzauza mapiri kuti, ‘Tikwirireni!’ Adzauzanso mapiri angʼonoangʼono kuti, ‘Tigwereni!’+