Hoseya 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu Aisiraeli, mwakhala mukuchimwa kuyambira pa nthawi ya zochitika za ku Gibeya.+ Kumeneko anthu anapitirizabe kuchimwa. Nkhondo sinawononge anthu onse osalungama ku Gibeya.
9 Inu Aisiraeli, mwakhala mukuchimwa kuyambira pa nthawi ya zochitika za ku Gibeya.+ Kumeneko anthu anapitirizabe kuchimwa. Nkhondo sinawononge anthu onse osalungama ku Gibeya.