Hoseya 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mwalima zoipa,Ndipo mwakolola zosalungama.+Mwadya zipatso za chinyengo chanu.Chifukwa mukudalira njira zanu,Ndiponso kuchuluka kwa asilikali anu. Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:13 Tsiku la Yehova, ptsa. 157-158
13 Koma mwalima zoipa,Ndipo mwakolola zosalungama.+Mwadya zipatso za chinyengo chanu.Chifukwa mukudalira njira zanu,Ndiponso kuchuluka kwa asilikali anu.