Hoseya 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakati pa anthu a mtundu wanu padzakhala chisokonezo.Ndipo mizinda yanu yonse yokhala ndi mipanda yolimba idzawonongedwa,+Ngati mmene Salimani anawonongera Beti-aribeliPa tsiku lankhondo, pamene azimayi ndi ana awo anawanyenyanyenya.
14 Pakati pa anthu a mtundu wanu padzakhala chisokonezo.Ndipo mizinda yanu yonse yokhala ndi mipanda yolimba idzawonongedwa,+Ngati mmene Salimani anawonongera Beti-aribeliPa tsiku lankhondo, pamene azimayi ndi ana awo anawanyenyanyenya.