Hoseya 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu anthu a ku Beteli, wina adzakuchitaninso zimenezi+ chifukwa ndinu oipa kwambiri. Ndithu, mfumu ya Isiraeli idzawonongedwa* mʼbandakucha.”+
15 Inu anthu a ku Beteli, wina adzakuchitaninso zimenezi+ chifukwa ndinu oipa kwambiri. Ndithu, mfumu ya Isiraeli idzawonongedwa* mʼbandakucha.”+