Hoseya 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamene iwo* ankawaitana kwambiri,Mʼpamenenso iwo ankawathawa kwambiri.+ Ankapereka nsembe kwa zifaniziro za Baala,+Ndipo nsembezo ankaziperekanso kwa zifaniziro zogoba.+
2 Pamene iwo* ankawaitana kwambiri,Mʼpamenenso iwo ankawathawa kwambiri.+ Ankapereka nsembe kwa zifaniziro za Baala,+Ndipo nsembezo ankaziperekanso kwa zifaniziro zogoba.+