Hoseya 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu anga atsimikiza kuti akhale osakhulupirika kwa ine.+ Ngakhale kuti anawaitanira kumwamba,* palibe amene anaimirira.
7 Anthu anga atsimikiza kuti akhale osakhulupirika kwa ine.+ Ngakhale kuti anawaitanira kumwamba,* palibe amene anaimirira.