Hoseya 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Sindidzasonyeza mkwiyo wanga woyaka moto. Sindidzawononganso Efuraimu+Chifukwa ndine Mulungu, osati munthu.Ndine Woyera pakati panu,Ndipo sindidzabwera kwa inu nditakwiya.
9 Sindidzasonyeza mkwiyo wanga woyaka moto. Sindidzawononganso Efuraimu+Chifukwa ndine Mulungu, osati munthu.Ndine Woyera pakati panu,Ndipo sindidzabwera kwa inu nditakwiya.