Hoseya 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo adzatsatira Yehova ndipo iye adzabangula ngati mkango.+Ndipo akadzabangula, ana ake adzabwera akunjenjemera kuchokera kumadzulo.+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:10 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 156
10 Iwo adzatsatira Yehova ndipo iye adzabangula ngati mkango.+Ndipo akadzabangula, ana ake adzabwera akunjenjemera kuchokera kumadzulo.+