Hoseya 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Efuraimu amandiuza mabodza okhaokha.Kulikonse kumene ndingayangʼane, ndikuona chinyengo cha Isiraeli.+ Koma Yuda akuyendabe ndi Mulungu,Ndipo iye ndi wokhulupirika kwa Woyera Koposa.”+
12 “Efuraimu amandiuza mabodza okhaokha.Kulikonse kumene ndingayangʼane, ndikuona chinyengo cha Isiraeli.+ Koma Yuda akuyendabe ndi Mulungu,Ndipo iye ndi wokhulupirika kwa Woyera Koposa.”+