Hoseya 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho iwo adzakhala ngati mitambo ya mʼmawa,Ndiponso ngati mame amene sachedwa kuuma.Adzakhalanso ngati mankhusu* amene amauluzika ndi mphepo kuchokera pamalo opunthira mbewu,Ndiponso ngati utsi umene umatuluka mʼchumuni kudenga.
3 Choncho iwo adzakhala ngati mitambo ya mʼmawa,Ndiponso ngati mame amene sachedwa kuuma.Adzakhalanso ngati mankhusu* amene amauluzika ndi mphepo kuchokera pamalo opunthira mbewu,Ndiponso ngati utsi umene umatuluka mʼchumuni kudenga.