Hoseya 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma ine ndine Yehova Mulungu wako kuchokera pamene unali ku Iguputo.+Palibe Mulungu wina amene unkamudziwa kupatula ine.Palibenso mpulumutsi wina kupatula ine.+
4 Koma ine ndine Yehova Mulungu wako kuchokera pamene unali ku Iguputo.+Palibe Mulungu wina amene unkamudziwa kupatula ine.Palibenso mpulumutsi wina kupatula ine.+