Hoseya 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iwe unakhuta chifukwa unali ndi zakudya zambiri.+Unakhuta ndipo mtima wako unayamba kunyada. Choncho unandiiwala.+ Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:6 Tsiku la Yehova, ptsa. 61, 158-159
6 Iwe unakhuta chifukwa unali ndi zakudya zambiri.+Unakhuta ndipo mtima wako unayamba kunyada. Choncho unandiiwala.+