-
Hoseya 13:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndidzawaukira ngati chimbalangondo chimene ana ake asowa,
Ndipo ndidzawangʼamba pachifuwa,
Kumeneko ndidzawadya ngati mkango.
Chilombo chakutchire chidzawakhadzulakhadzula.
-