Hoseya 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiye ili kuti mfumu yako, kuti ikupulumutse mʼmizinda yako yonse?+Olamulira* ako ali kuti amene unawauza kuti,‘Ndipatseni mfumu ndiponso akalongaʼ?+
10 Ndiye ili kuti mfumu yako, kuti ikupulumutse mʼmizinda yako yonse?+Olamulira* ako ali kuti amene unawauza kuti,‘Ndipatseni mfumu ndiponso akalongaʼ?+