Hoseya 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ine ndidzawombola anthu anga ku mphamvu za Manda.*Ndidzawapulumutsa ku imfa.+ Iwe Imfa amene umabweretsa ululu woopsa, kodi mphamvu yako ili kuti?+ Iwe Manda, kodi mphamvu yako yowononga ili kuti?+ Koma Efuraimu sindimumvera chisoni. Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:14 Nsanja ya Olonda,11/15/2005, tsa. 292/15/1995, tsa. 103/1/1989, ptsa. 14-15
14 Ine ndidzawombola anthu anga ku mphamvu za Manda.*Ndidzawapulumutsa ku imfa.+ Iwe Imfa amene umabweretsa ululu woopsa, kodi mphamvu yako ili kuti?+ Iwe Manda, kodi mphamvu yako yowononga ili kuti?+ Koma Efuraimu sindimumvera chisoni.