Hoseya 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngakhale atakula bwino pakati pa bango,Mphepo yakumʼmawa idzabwera, mphepo ya Yehova.Idzabwera kuchokera kuchipululu nʼkuumitsa chitsime chake ndi kasupe wake. Winawake adzawononga chuma chake chonse chamtengo wapatali.+
15 Ngakhale atakula bwino pakati pa bango,Mphepo yakumʼmawa idzabwera, mphepo ya Yehova.Idzabwera kuchokera kuchipululu nʼkuumitsa chitsime chake ndi kasupe wake. Winawake adzawononga chuma chake chonse chamtengo wapatali.+