Hoseya 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Samariya adzaimbidwa mlandu+ chifukwa wagalukira Mulungu wake.+ Iwo adzagwetsedwa ndi lupanga.+Ana awo adzaphwanyidwaphwanyidwa.Ndipo akazi awo apakati adzatumbulidwa.” Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:16 Nsanja ya Olonda,11/15/2005, ptsa. 29-30
16 Samariya adzaimbidwa mlandu+ chifukwa wagalukira Mulungu wake.+ Iwo adzagwetsedwa ndi lupanga.+Ana awo adzaphwanyidwaphwanyidwa.Ndipo akazi awo apakati adzatumbulidwa.”