Hoseya 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Inu Aisiraeli, bwererani kwa Yehova Mulungu wanu,+Popeza mwapunthwa chifukwa cha zolakwa zanu.