Hoseya 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Bwererani kwa Yehova ndi mawu amenewa.Uzani Mulungu kuti, ‘Tikhululukireni zolakwa zathu.+ Landirani zinthu zathu zabwino,Ndipo tidzakutamandani ndi pakamwa pathu+ ngati mmene tingaperekere nsembe kwa inu ana a ngʼombe amphongo. Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:2 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,10/2017, tsa. 6 Nsanja ya Olonda,2/15/2011, tsa. 164/1/2007, tsa. 2011/15/2005, ptsa. 30-3112/15/1989, ptsa. 20-21 Tsiku la Yehova, ptsa. 167-168, 177-178
2 Bwererani kwa Yehova ndi mawu amenewa.Uzani Mulungu kuti, ‘Tikhululukireni zolakwa zathu.+ Landirani zinthu zathu zabwino,Ndipo tidzakutamandani ndi pakamwa pathu+ ngati mmene tingaperekere nsembe kwa inu ana a ngʼombe amphongo.
14:2 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,10/2017, tsa. 6 Nsanja ya Olonda,2/15/2011, tsa. 164/1/2007, tsa. 2011/15/2005, ptsa. 30-3112/15/1989, ptsa. 20-21 Tsiku la Yehova, ptsa. 167-168, 177-178