Hoseya 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Efuraimu adzanena kuti, ‘Mafano alibenso ntchito kwa ine.’+ Ine ndidzamva ndipo ndidzamuyangʼanira.+ Ndidzakhala ngati mtengo wa mkungudza wobiriwira bwino. Ndipo mudzapeza zipatso kwa ine.”
8 Efuraimu adzanena kuti, ‘Mafano alibenso ntchito kwa ine.’+ Ine ndidzamva ndipo ndidzamuyangʼanira.+ Ndidzakhala ngati mtengo wa mkungudza wobiriwira bwino. Ndipo mudzapeza zipatso kwa ine.”