Hoseya 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndani ali ndi nzeru? Amvetse zinthu zimenezi. Wochenjera ndani? Adziwe zimenezi. Njira za Yehova ndi zowongoka.+Ndipo anthu olungama adzayendamo,Koma olakwa adzapunthwa mʼnjira zimenezo. Hoseya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:9 Tsiku la Yehova, ptsa. 87-88 Nsanja ya Olonda,11/15/2005, tsa. 31
9 Ndani ali ndi nzeru? Amvetse zinthu zimenezi. Wochenjera ndani? Adziwe zimenezi. Njira za Yehova ndi zowongoka.+Ndipo anthu olungama adzayendamo,Koma olakwa adzapunthwa mʼnjira zimenezo.