Yoweli 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zinthu zimene ziwala zowononga zinasiya zinadyedwa ndi dzombe lambirimbiri.+Zimene dzombelo linasiya zinadyedwa ndi ana a dzombe opanda mapiko.Ndipo zimene ana a dzombe opanda mapiko anasiya zinadyedwa ndi dzombe losakaza.+ Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:4 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2020, ptsa. 2-3 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, ptsa. 8-95/1/1992, tsa. 11
4 Zinthu zimene ziwala zowononga zinasiya zinadyedwa ndi dzombe lambirimbiri.+Zimene dzombelo linasiya zinadyedwa ndi ana a dzombe opanda mapiko.Ndipo zimene ana a dzombe opanda mapiko anasiya zinadyedwa ndi dzombe losakaza.+
1:4 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2020, ptsa. 2-3 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, ptsa. 8-95/1/1992, tsa. 11