Yoweli 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munda wawonongedwa ndipo nthaka ikulira.+Mbewu zawonongedwa, vinyo watsopano watha ndipo mafuta sakupezekanso.+ Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:10 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, tsa. 10
10 Munda wawonongedwa ndipo nthaka ikulira.+Mbewu zawonongedwa, vinyo watsopano watha ndipo mafuta sakupezekanso.+