Yoweli 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Lengezani nthawi yosala kudya. Itanitsani msonkhano wapadera.+ Sonkhanitsani akulu ndi anthu onse okhala mʼdzikoli,Kuti akumane kunyumba ya Yehova Mulungu wanu+ ndipo alirire Yehova kuti awathandize. Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:14 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, ptsa. 10-11
14 Lengezani nthawi yosala kudya. Itanitsani msonkhano wapadera.+ Sonkhanitsani akulu ndi anthu onse okhala mʼdzikoli,Kuti akumane kunyumba ya Yehova Mulungu wanu+ ndipo alirire Yehova kuti awathandize.