Yoweli 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mudzadziwa kuti ine ndili pakati pa Isiraeli,+Komanso kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu+ ndipo palibenso wina. Anthu anga sadzachitanso manyazi mpaka kalekale. Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:27 Nsanja ya Olonda,5/1/1992, tsa. 13
27 Mudzadziwa kuti ine ndili pakati pa Isiraeli,+Komanso kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu+ ndipo palibenso wina. Anthu anga sadzachitanso manyazi mpaka kalekale.