Yoweli 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ankachitira maere anthu anga.+Ankagulitsa mnyamata kuti alipire hule,Ndipo ankagulitsa mtsikana kuti agule vinyo woti amwe. Yoweli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:3 Nsanja ya Olonda,5/1/1998, tsa. 22
3 Ankachitira maere anthu anga.+Ankagulitsa mnyamata kuti alipire hule,Ndipo ankagulitsa mtsikana kuti agule vinyo woti amwe.